1 Samueli 17:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo anali ndi chisoti chamkuwa pamutu pake, navala malaya aunyolo, olemera ngati masekeli zikwi zisanu za mkuwa, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo anali ndi chisoti chamkuwa pamutu pake, navala malaya aunyolo, olemera ngati masekeli zikwi zisanu za mkuwa, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ankavala chisoti chamkuŵa ndi malaya achitsulo, amene kulemera kwake kunali ngati makilogramu 57. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Iye ankavala chipewa chamkuwa ndi malaya achitsulo olemera makilogalamu 57. Onani mutuwo |