1 Samueli 17:6 - Buku Lopatulika6 nakuta msongolo wake ndi chovala chamkuwa, ndiponso pachikota pake panali nthungo yamkuwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 nakuta msongolo wake ndi chovala chamkuwa, ndiponso pachikota pake panali nthungo yamkuwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ankavalanso zokuta miyendo yake zamkuŵa, ndipo ankanyamula nthungo yamkuŵa pa phewa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ankavalanso zokuta miyendo yake zamkuwa, ndipo ankanyamula nthungo ya mkuwa pa phewa pake. Onani mutuwo |