1 Samueli 17:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo Davide anati kwa Saulo, Asade nkhawa munthu aliyense chifukwa cha iyeyo; ine kapolo wanu ndidzapita kuponyana ndi Mfilisti uyu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo Davide anati kwa Saulo, Asade nkhawa munthu aliyense chifukwa cha iyeyo; ine kapolo wanu ndidzapita kuponyana ndi Mfilisti uyu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Tsono Davide adauza Saulo kuti, “Munthu aliyense asataye mtima chifukwa cha Mfilistiyu. Ineyo mnyamata wanune ndipita kukamenyana naye.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Davide anati kwa Sauli, “Munthu aliyense asataye mtima chifukwa cha Mfilisitiyu. Ine kapolo wanu ndipita kukamenyana naye.” Onani mutuwo |