1 Samueli 17:33 - Buku Lopatulika33 Ndipo Saulo anati kwa Davide, Sukhoza iwe kukomana ndi Mfilisti uyu kukaponyana naye; pakuti iwe ndiwe mnyamata, koma iye anazolowera nkhondo kuyambira ubwana wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201433 Ndipo Saulo anati kwa Davide, Sukhoza iwe kukomana ndi Mfilisti uyu kukaponyana naye; pakuti iwe ndiwe mnyamata, koma iye anazolowera nkhondo kuyambira ubwana wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa33 Saulo adamuuza kuti, “Sungathe kukamenyana naye Mfilistiyu, pakuti iwe ndiwe mnyamata, koma iyeyu ndi munthu wozoloŵera kumenya nkhondo kuyambira ubwana wake.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero33 Sauli anayankha Davide kuti, “Iwe sungathe kupita kukamenyana ndi Mfilisitiyu. Iwe ukanali mnyamata, koma iyeyu ndi amene wakhala akumenya nkhondo kuyambira unyamata wake.” Onani mutuwo |