1 Samueli 17:31 - Buku Lopatulika31 Ndipo pamene mau adanena Davide anamveka, anawapitiriza kwa Saulo; ndipo iye anamuitana. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 Ndipo pamene mau adanena Davide anamveka, anawapitiriza kwa Saulo; ndipo iye anamuitana. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Mau amene ankalankhula Davide aja atamveka, anthu adakafotokozera Saulo, ndipo Sauloyo adamuitanitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Mawu amene Davide anayankhula atamveka, anthu anakafotokozera Sauli ndipo Sauli anamuyitanitsa. Onani mutuwo |