1 Samueli 17:30 - Buku Lopatulika30 Napotolokera iye kwa munthu wina, nalankhula mau omwewo; ndipo anthu anamyankhanso monga momwemo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 Napotolokera iye kwa munthu wina, nalankhula mau omwewo; ndipo anthu anamyankhanso monga momwemo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Tsono adachoka apo napita kwa wina namufunsa zokhazokhazo. Aliyense adamuyankhanso monga poyamba paja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Ndipo anamuchokera napita kwa munthu wina ndipo anamufunsa nkhani yomweyo, ndipo anthu anamuyankha iye monga poyamba paja. Onani mutuwo |