1 Samueli 17:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo Afilisti anaima paphiri tsidya lija, ndi Aisraele anaima paphiri tsidya lina; ndi pakati pao panali chigwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo Afilisti anaima paphiri tsidya lija, ndi Aisraele anaima paphiri tsidya lina; ndi pakati pao panali chigwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Afilisti ndi Aisraele adaika ankhondo ao moyang'anana, ena mbali ina paphiri, ena mbali ina paphirinso, pakatipa chigwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Afilisti anali phiri lina ndipo Aisraeli analinso phiri lina, ndipo pakati pawo panali chigwa. Onani mutuwo |