1 Samueli 17:3 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Afilisti anali phiri lina ndipo Aisraeli analinso phiri lina, ndipo pakati pawo panali chigwa. Onani mutuwoBuku Lopatulika3 Ndipo Afilisti anaima paphiri tsidya lija, ndi Aisraele anaima paphiri tsidya lina; ndi pakati pao panali chigwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo Afilisti anaima paphiri tsidya lija, ndi Aisraele anaima paphiri tsidya lina; ndi pakati pao panali chigwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Afilisti ndi Aisraele adaika ankhondo ao moyang'anana, ena mbali ina paphiri, ena mbali ina paphirinso, pakatipa chigwa. Onani mutuwo |