1 Samueli 17:15 - Buku Lopatulika15 Koma Davide akamuka kwa Saulo, nabwerera kudzadyetsa nkhosa za atate wake ku Betelehemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Koma Davide akamuka kwa Saulo, nabwerera kudzadyetsa nkhosa za atate wake ku Betelehemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Koma Davide ankapita ku zithando za Saulo, namabwerako nthaŵi zina kukaŵeta nkhosa za bambo wake ku Betelehemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Koma Davide ankapita ku misasa ya Sauli ndi kubwerako kuti azikaweta nkhosa za abambo ake ku Betelehemu. Onani mutuwo |