1 Samueli 17:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo Mfilistiyo anayandikira m'mawa ndi madzulo, nadzionetsera masiku makumi anai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo Mfilistiyo anayandikira m'mawa ndi madzulo, nadzionetsera masiku makumi anai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Pa masiku makumi anai Goliyati uja adakhala akutuluka, namadziwonetsa m'maŵa ndi madzulo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Kwa masiku makumi anayi, Mfilisiti uja ankabwera mmawa ndi madzulo kumadzionetsera. Onani mutuwo |