Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 17:14 - Buku Lopatulika

14 Ndipo Davide anali wotsiriza; ndi akulu atatuwo anamtsata Saulo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Ndipo Davide anali wotsiriza; ndi akulu atatuwo anamtsata Saulo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Davide anali mzime. Ana akuluakulu atatuwo ndiwo anali ku nkhondo ndi Saulo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Davide ndiye anali mzime. Ana aakulu atatuwo ndiwo anapita ku nkhondo ndi Sauli.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 17:14
3 Mawu Ofanana  

Yehova ndipo anati kwa iye, Mitundu iwiri ili m'mimba mwako, magulu awiri a anthu adzatuluka m'mimba mwako; gulu lina lidzapambana mphamvu ndi linzake; wamkulu adzakhala kapolo wa wamng'ono.


Ndipo Samuele anati kwa Yese, Ana anu ndi omwewa kodi? Nati iye, Watsala wina, mng'ono wa onse, ndipo taonani, iye alikuweta nkhosa. Ndipo Samuele anati kwa Yese, Tumiza munthu akamtenge; pakuti ife sitidzakhala pansi kufikira iye atadza kuno.


Koma Davide akamuka kwa Saulo, nabwerera kudzadyetsa nkhosa za atate wake ku Betelehemu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa