1 Samueli 16:9 - Buku Lopatulika9 Pamenepo Yese anapititsapo Sama. Ndipo anati, Koma uyunso Yehova sanamsankhe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pamenepo Yese anapititsapo Sama. Ndipo anati, Koma uyunso Yehova sanamsankhe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pamenepo Yese adaitana Sama kuti apite kwa Samuele. Koma Samuele adati, “Ameneyunso Chauta sadamsankhe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ndipo Yese anayitana Sama, koma Samueli anati, “Ngakhale uyu Yehova sanamusankhe.” Onani mutuwo |