1 Samueli 16:8 - Buku Lopatulika8 Pamenepo Yese anaitana Abinadabu nampititsa pa Samuele. Ndipo iye adati, Koma uyunso Yehova sadamsankhe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Pamenepo Yese anaitana Abinadabu nampititsa pa Samuele. Ndipo iye adati, Koma uyunso Yehova sadamsankhe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono Yese adaitana Abinadabu namtumiza kwa Samuele. Ndipo Samuele adati, “Ameneyunso Chauta sadamsankhe.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Kenaka Yese anayitana Abinadabu namubweretsa pamaso pa Samueli. Koma Samueli anati, “Yehova sanamusankhenso ameneyu.” Onani mutuwo |