1 Samueli 16:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Yese anapititsapo ana ake aamuna asanu ndi awiri. Koma Samuele anati kwa Yese, Yehova sanawasankhe awa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Yese anapititsapo ana ake amuna asanu ndi awiri. Koma Samuele anati kwa Yese, Yehova sanawasankhe awa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Choncho Yese adatumiza ana ake aamuna asanu ndi aŵiri kuti apite kwa Samuele. Koma Samueleyo adati, “Chauta sadaŵasankhe ameneŵa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Pambuyo pake, Yese anayitana ana ake amuna asanu ndi awiri kuti apite kwa Samueli. Koma Samueli anati, “Yehova sanasankhe amenewa.” Onani mutuwo |