1 Samueli 16:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo kunali, pakufika iwo, iye anayang'ana pa Eliyabu, nati, Zoonadi, wodzozedwa wa Yehova ali pamaso pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo kunali, pakufika iwo, iye anayang'ana pa Eliyabu, nati, Zoonadi, wodzozedwa wa Yehova ali pamaso pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Onsewo atafika, Samuele adayang'ana Eliyabu namaganiza kuti, “Ndithudi amene Chauta adamsankha ndi uyu ali pamaso pakeyu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Pamene anafika, Samueli anaona Eliabu ndipo anaganiza “Ndithu wodzozedwa wa Yehova uja ndi uyu wayima pamaso pakeyu.” Onani mutuwo |