1 Samueli 16:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Samuele anachita chimene Yehova ananena, nadza ku Betelehemu. Ndipo akulu a mzindawo anadza kukomana naye monthunthumira, nati, Mubwera ndi mtendere kodi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Samuele anachita chimene Yehova ananena, nadza ku Betelehemu. Ndipo akulu a mudziwo anadza kukomana naye monthunthumira, nati, Mubwera ndi mtendere kodi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Samuele adachitadi zimene Chauta adalamula, nakafika ku Betelehemu. Atsogoleri amumzindamo adadzamchingamira ali njenjenje, ndipo adamufunsa kuti, “Kodi nkwabwino?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Samueli anachita zimene Yehova ananena, ndipo anabweradi ku Betelehemu kuja. Akuluakulu a mu mzindawo anamuchingamira ali njenjenje ndi mantha ndipo anamufunsa kuti, “Kodi mwabwera mwa mtendere?” Onani mutuwo |