1 Samueli 16:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo Saulo anatumiza kwa Yese, nati, Ulole kuti Davide aime pamaso panga; pakuti ndamkomera mtima. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo Saulo anatumiza kwa Yese, nati, Ulole kuti Davide aime pamaso panga; pakuti ndamkomera mtima. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Kenaka Saulo adatumiza mau kwa Yese kuti, “Davide akhale womanditumikira, pakuti ndamkonda kwambiri.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Kenaka Sauli anatumiza mawu kwa Yese ndi kuti, “Mulole kuti Davide azinditumikira, pakuti ndamukonda kwambiri.” Onani mutuwo |