1 Samueli 16:20 - Buku Lopatulika20 Ndipo Yese anatenga bulu namsenza mkate, ndi thumba la vinyo, ndi mwanawambuzi, nazitumiza kwa Saulo ndi Davide mwana wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndipo Yese anatenga bulu namsenza mkate, ndi thumba la vinyo, ndi mwanawambuzi, nazitumiza kwa Saulo ndi Davide mwana wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Yese adatenga bulu namsenzetsa buledi, thumba lachikopa la vinyo ndi mwanawambuzi. Zonsezo adapatsa Davide mwana wake, kuti akazipereke kwa Saulo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Choncho Yese anatenga bulu namunyamulitsa buledi, thumba la vinyo ndi mwana wambuzi mmodzi. Zonsezi anamupatsa mwana wake Davide kuti akapereke kwa Sauli. Onani mutuwo |