1 Samueli 16:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo mnyamata wake wina anayankha, nati, Taonani, ine ndaona mwana wa Yese wa ku Betelehemu, ndiye wanthetemya wodziwa kuimbira, ndipo ali wa mtima wolimba ndi woyenera nkhondo, ndiponso ali wochenjera manenedwe ake; ndiye munthu wokongola, ndipo Yehova ali naye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo mnyamata wake wina anayankha, nati, Taonani, ine ndaona mwana wa Yese wa ku Betelehemu, ndiye wanthetemya wodziwa kuimbira, ndipo ali wa mtima wolimba ndi woyenera nkhondo, ndiponso ali wochenjera manenedwe ake; ndiye munthu wokongola, ndipo Yehova ali naye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Mmodzi mwa antchitowo adati, “Ndaona mwana wamwamuna wa Yese wa ku Betelehemu amene ali wokhoza zeze, munthu wolimba mtima, ngwazi pankhondo, wochenjera polankhula, munthu wokongola. Ndipo Chauta ali naye.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Mmodzi mwa antchito ake anati, “Ine ndinaona mwana wa Yese wa ku Betelehemu. Ndiye munthu wodziwa bwino kuyimba, wolimba mtima, ngwazi pa nkhondo, wodziwa kuyankhula ndi wokongola. Ndipotu Yehova ali ndi iye.” Onani mutuwo |