Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 16:17 - Buku Lopatulika

17 Ndipo Saulo anati kwa anyamata ake, Mundifunire tsono munthu wakudziwa kuimba bwino, nimubwere naye kwa ine.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndipo Saulo anati kwa anyamata ake, Mundifunire tsono munthu wakudziwa kuimba bwino, nimubwere naye kwa ine.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Pamenepo Saulo adaŵauza kuti, “Chabwino mundifunire munthu wodziŵa bwino kuimba kwake, ndipo mubwere naye kuno.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Choncho Sauli anati kwa atumiki ake, “Chabwino, kandipezereni munthu wodziwa bwino kuyimba ndipo mubwere naye kuno.”

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 16:17
2 Mawu Ofanana  

Tsono inu mbuye wathu muuze anyamata anu, amene ali pamaso panu, kuti afune munthu wanthetemya wodziwa kuimba zeze; ndipo kudzakhala, pamene mzimu woipa wochokera kwa Mulungu uli pa inu, iyeyo adzaimba ndi dzanja lake, ndipo mudzakhala wolama.


Ndipo mnyamata wake wina anayankha, nati, Taonani, ine ndaona mwana wa Yese wa ku Betelehemu, ndiye wanthetemya wodziwa kuimbira, ndipo ali wa mtima wolimba ndi woyenera nkhondo, ndiponso ali wochenjera manenedwe ake; ndiye munthu wokongola, ndipo Yehova ali naye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa