1 Samueli 16:16 - Buku Lopatulika16 Tsono inu mbuye wathu muuze anyamata anu, amene ali pamaso panu, kuti afune munthu wanthetemya wodziwa kuimba zeze; ndipo kudzakhala, pamene mzimu woipa wochokera kwa Mulungu uli pa inu, iyeyo adzaimba ndi dzanja lake, ndipo mudzakhala wolama. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Tsono inu mbuye wathu muuze anyamata anu, amene ali pamaso panu, kuti afune munthu wanthetemya wodziwa kuimba zeze; ndipo kudzakhala, pamene mzimu woipa wochokera kwa Mulungu uli pa inu, iyeyo adzaimba ndi dzanja lake, ndipo mudzakhala wolama. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Ndiye inu mbuyathu, tilamuleni antchito anufe pano kuti tifunefune munthu waluso poimba zeze. Mzimu woipawu ukakufikirani, munthuyo azidzaimba zeze, ndipo mudzapeza bwino.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Ndiyetu, inu mbuye wathu titumeni ife antchito anu kuti tikafune munthu wodziwa bwino kuyimba zeze. Tsono pamene mzimu woyipa wochokera kwa Mulungu wakufikirani, iye azidzayimba ndipo mudzakhala bwino.” Onani mutuwo |