1 Samueli 15:8 - Buku Lopatulika8 Namtenga wamoyo Agagi, mfumu ya Aamaleke, naononga konsekonse anthu onse ndi lupanga lakuthwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Namtenga wamoyo Agagi, mfumu ya Aamaleke, naononga konsekonse anthu onse ndi lupanga lakuthwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Adamtenga wamoyo Agagi, mfumu ya Aamaleke, ndipo adapha anthu ena onse ndi lupanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Sauli anatenga Agagi mfumu ya Aamaleki, koma anthu ake onse anawapha ndi lupanga. Onani mutuwo |