1 Samueli 15:34 - Buku Lopatulika34 Pamenepo Samuele ananka ku Rama; ndi Saulo anakwera kunka kunyumba yake ku Gibea wa Saulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Pamenepo Samuele ananka ku Rama; ndi Saulo anakwera kunka kunyumba yake ku Gibea wa Saulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Tsono Samuele adapita ku Rama, koma Saulo adapita ku nyumba yake ku Gibea wa Saulo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Ndipo Samueli anapita ku Rama, koma Sauli anapita ku mudzi kwawo ku Gibeya wa Sauli. Onani mutuwo |