1 Samueli 15:35 - Buku Lopatulika35 Ndipo Samuele sanadzenso kudzaona Saulo kufikira tsiku la imfa yake; koma Samuele analira chifukwa cha Saulo; ndipo Yehova anali ndi chisoni kuti anamlonga Saulo mfumu ya Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201435 Ndipo Samuele sanadzenso kudzaona Saulo kufikira tsiku la imfa yake; koma Samuele analira chifukwa cha Saulo; ndipo Yehova anali ndi chisoni kuti anamlonga Saulo mfumu ya Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa35 Samuele sadamuwonenso Saulo moyo wake wonse, koma ankamulira ndithu, popeza kuti Chauta adaamuchotsa Sauloyo kukhala mfumu yolamulira Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero35 Samueli sanamuonenso Sauli mpaka imfa yake ngakhale kuti ankamulira Sauliyo. Yehova anamva chisoni kuti anasankha Sauli kuti akhale mfumu ya Israeli. Onani mutuwo |