1 Samueli 15:29 - Buku Lopatulika29 Ndiponso Wamphamvu wa Israele sanama kapena kulapa; popeza Iye sali munthu kuti akalapa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndiponso Wamphamvu wa Israele sanama kapena kulapa; popeza Iye sali munthu kuti akalapa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Mulungu Waulemerero wa Aisraele sanama kapena kusintha maganizo. Pakuti Iye si munthu, kuti athe kusintha maganizo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Mulungu wa ulemerero wa Israeli sanama kapena kusintha maganizo ake; pakuti iye si munthu, kuti asinthe maganizo ake.” Onani mutuwo |