1 Samueli 15:18 - Buku Lopatulika18 Ndipo Yehova anakutumani ulendo, kuti, Muka, nuononge konsekonse Aamaleke akuchita zoipawo, nuponyane nao kufikira utawatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndipo Yehova anakutumani ulendo, kuti, Muka, nuononge konsekonse Aamaleke akuchita zoipawo, nuponyane nao kufikira utawatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ndipo Chauta adakutumani kuti, ‘Pita, ukaononge kwathunthu Aamaleke, anthu oipa mtima aja, ndipo uchite nawo nkhondo mpaka kuŵatheratu onsewo.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ndipo Yehova anakutumani kuti, ‘Pitani mukawononge kwathunthu Aamaleki, anthu oyipa aja. Mukachite nawo nkhondo mpaka kuwatheratu.’ Onani mutuwo |