1 Samueli 15:17 - Buku Lopatulika17 Nati Samuele, M'mene munali wamng'ono m'maso a inu nokha, kodi simunaikidwe mutu wa mafuko a Israele? Ndipo Yehova anakudzozani mfumu ya Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Nati Samuele, M'mene munali wamng'ono m'maso a inu nokha, kodi simunaikidwa mutu wa mafuko a Israele? Ndipo Yehova anakudzozani mfumu ya Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Samuele adati, “Ngakhale kale munali wamng'ono pamaso pa anthu, tsopano mwasanduka mtsogoleri wa mafuko onse a Aisraele. Chauta adakudzozani kuti mukhale mfumu yomalamulira Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Apo Samueli anati, “Munali wamngʼono pa maso pa anthu, koma tsopano mwasanduka mtsogoleri wa mafuko a Israeli. Yehova anakudzozani kuti mukhale mfumu yolamulira Aisraeli. Onani mutuwo |