1 Samueli 15:19 - Buku Lopatulika19 Chifukwa ninji tsono simunamvere mau a Yehova, koma munathamangira zowawanya, ndi kuchita choipa pamaso pa Yehova? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Chifukwa ninji tsono simunamvera mau a Yehova, koma munathamangira zowawanya, ndi kuchita choipa pamaso pa Yehova? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Chifukwa chiyani nanga simudamvere mau a Chauta? Chifukwa chiyani mudathamangira zofunkha ndi kuchita zoipira Chauta?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Chifukwa chiyani simunamvere mawu a Yehova? Chifukwa chiyani munathamangira zofunkha ndi kuchita choyipira Yehova?” Onani mutuwo |