1 Samueli 15:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo Saulo anati, Anazitenga kwa Aamaleke; pakuti anthu anasunga nkhosa zokometsetsa ndi ng'ombe, kuzipereka nsembe kwa Yehova Mulungu wanu; koma zina tinaziononga konsekonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo Saulo anati, Anazitenga kwa Aamaleke; pakuti anthu anasunga nkhosa zokometsetsa ndi ng'ombe, kuzipereka nsembe kwa Yehova Mulungu wanu; koma zina tinaziononga konsekonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Saulo adayankha kuti, “Zimenezi adakazitenga kwa Aamaleke, pakuti anthu adasungako nkhosa ndi ng'ombe zabwino koposa, kuti akapereke nsembe kwa Chauta, Mulungu wanu. Koma zina zonse taziwononga kotheratu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Sauli anayankha, “Zimenezi Asilikali azitenga kuchokera kwa Aamaleki. Iwo anasungako nkhosa ndi ngʼombe zabwino kuti akapereke nsembe kwa Yehova Mulungu wanu, koma zina zonse anaziwononga.” Onani mutuwo |