1 Samueli 15:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo Samuele anati, Koma tsono kulirako kwa nkhosa ndilikumva m'makutu anga, ndi kulirako kwa ng'ombe ndilikumva, nchiyani? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo Samuele anati, Koma tsono kulirako kwa nkhosa ndilikumva m'makutu anga, ndi kulirako kwa ng'ombe ndilikumva, nchiyani? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Koma Samuele adati, “Nanga bwanji ndikumva nkhosa ndi ng'ombe zikulira?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Koma Samueli anati, “Nanga bwanji ndikumva kulira kwa nkhosa ndi ngʼombe?” Onani mutuwo |