1 Samueli 15:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo Samuele anadza kwa Saulo; ndipo Saulo anati kwa iye, Yehova akudalitseni; ine ndinachita lamulo la Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo Samuele anadza kwa Saulo; ndipo Saulo anati kwa iye, Yehova akudalitseni; ine ndinachita lamulo la Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Samuele atafika kwa Saulo, Sauloyo adamuuza kuti, “Chauta akudalitseni. Ndachitadi zonse zimene Chauta adandilamula.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Samueli atamupeza Sauli, Sauliyo anati kwa Samueli, “Yehova akudalitseni! Ndachita zonse zimene Yehova analamula.” Onani mutuwo |