1 Samueli 15:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Samuele analawirira m'mawa kuti akakomane ndi Saulo; ndipo munthu anamuuza Samuele kuti, Saulo anafika ku Karimele, ndipo taonani, anaimika chikumbutso chake, nazungulira, napitirira, natsikira ku Giligala. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Samuele analawirira m'mawa kuti akakomane ndi Saulo; ndipo munthu anamuuza Samuele kuti, Saulo anafika ku Karimele, ndipo taonani, anaimika chikumbutso chake, nazungulira, napitirira, natsikira ku Giligala. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 M'mamaŵa ndithu, Samuele adadzuka kuti akakumane ndi Saulo. Anthu adamuuza kuti, “Saulo adabwera ku Karimele, ndipo kumeneko adadziimikira mwala wa chikumbutso cha iye mwini. Tsono adachokapo napitirira mpaka ku Giligala.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Samueli anadzuka mmamawa ndipo anapita kukakumana ndi Sauli. Koma anthu anamuwuza kuti, “Sauli anabwera ku Karimeli, ndipo kumeneko wadziyimikira mwala wachikumbutso cha iye mwini. Tsopano wachokako ndipo wapita ku Giligala.” Onani mutuwo |