1 Samueli 14:9 - Buku Lopatulika9 Akatero ndi ife kuti, Baimani kufikira titsikira kwa inu; tsono tidzaima m'malo mwathu, osakwera kwa iwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Akatero ndi ife kuti, Baimani kufikira titsikira kwa inu; tsono tidzaima m'malo mwathu, osakwera kwa iwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Akatiwuza kuti, ‘Dikirani mpaka tikupezeni,’ tikangoima pamalo pathu, osapita kwa iwowo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Akatiwuza kuti, ‘Imani pomwepo mpaka tikupezeni,’ ife tikangoyima pomwepo osapita kumene kuli iwoko. Onani mutuwo |