1 Samueli 14:10 - Buku Lopatulika10 Koma akatero kuti, Kwerani kuno kwa ife, tsono tidzakwera; pakuti Yehova wawapereka m'manja mwathu; ndipo ichi chidzatikhalira chizindikiro. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Koma akatero kuti, Kwerani kuno kwa ife, tsono tidzakwera; pakuti Yehova wawapereka m'manja mwathu; ndipo ichi chidzatikhalira chizindikiro. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Koma akanena kuti, ‘Bwerani kuno,’ ife tikapitadi, pakuti Chauta waapereka anthuwo m'manja mwathu. Chimenechi chidzakhala chizindikiro kwa ife.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Koma akadzati, ‘Bwerani kuno,’ ndiye ife tikapitedi, chifukwa ichi chidzakhala chizindikiro chakuti Yehova wapereka mʼmanja mwathu.” Onani mutuwo |