1 Samueli 14:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo Yonatani anati, Taona, ife tidzapita kunka kwa anthuwo, ndipo tidzadziwulula kwa iwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo Yonatani anati, Taona, ife tidzapita kunka kwa anthuwo, ndipo tidzadziwulula kwa iwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Tsono Yonatani adati, “Tiwolokere kwa anthuwo, ndipo tikadziwonetse kwa iwo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Yonatani anati, “Tiye tsono tiwoloke kupita kumene kuli anthuwo ndi kukadzionetsa kwa iwo. Onani mutuwo |