1 Samueli 14:48 - Buku Lopatulika48 Ndipo iye anakula mphamvu, nakantha Aamaleke, napulumutsa Aisraele m'manja a akuwawawanya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201448 Ndipo iye anakula mphamvu, nakantha Aamaleke, napulumutsa Aisraele m'manja a akuwawawanya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa48 Adachita zamphamvu, ndipo adagonjetsa Aamaleke. Motero adapulumutsa Aisraele kwa anthu amene ankaŵalanda zinthu zao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero48 Anachita nkhondo mwamphamvu ndi kugonjetsa Aamaleki. Choncho anapulumutsa Aisraeli mʼmanja mwa anthu amene ankawalanda zinthu zawo. Onani mutuwo |