1 Samueli 14:47 - Buku Lopatulika47 Ndipo pamene Saulo atakhazikitsa ufumu wa pa Israele, iye anaponyana ndi adani ake onse pozungulira ponse, ndi Mowabu, ndi ana a Amoni, ndi Edomu ndi mafumu a Zoba, ndi Afilisti; ndipo paliponse anapotolokerapo, anawalanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201447 Ndipo pamene Saulo atakhazikitsa ufumu wa pa Israele, iye anaponyana ndi adani ake onse pozungulira ponse, ndi Mowabu, ndi ana a Amoni, ndi Edomu ndi mafumu a Zoba, ndi Afilisti; ndipo paliponse anapotolokerapo, anawalanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa47 Pamene Saulo adakhala mfumu yolamulira Aisraele, adamenyana nkhondo ndi adani ake onse omzungulira. Adamenyana ndi Amowabu, Aamoni, Aedomu, mafumu a ku Zoba ndiponso Afilisti. Kulikonse kumene ankapita, ankaŵagonjetsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero47 Sauli ali mtsogoleri wa Israeli, anachita nkhondo ndi adani awa omuzungulira: Mowabu, Amoni, Edomu mafumu a ku Zoba ndi Afilisti. Kulikonse kumene ankapita ankawagonjetsa. Onani mutuwo |