Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 14:46 - Buku Lopatulika

46 Ndipo Saulo analeka kuwapirikitsa Afilistiwo; ndi Afilistiwo anamuka ku malo a iwo okha.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

46 Ndipo Saulo analeka kuwapirikitsa Afilistiwo; ndi Afilistiwo anamuka ku malo a iwo okha.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

46 Pambuyo pake Saulo adaleka kuŵathamangira Afilisti, ndipo Afilistiwo adabwerera kwao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

46 Pambuyo pake Sauli analeka kulondola Afilisti, kenaka anabwerera ku dziko lawo.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 14:46
3 Mawu Ofanana  

Ndipo anthuwo ananena ndi Saulo, kodi Yonatani adzafa, amene anachititsa chipulumutso chachikulu ichi mu Israele? Musatero. Pali Yehova, palibe tsitsi limodzi la pamutu wake lidzagwa pansi, pakuti iye anagwirizana ndi Mulungu lero. Chomwecho anthuwo anapulumutsa Yonatani kuti angafe.


Ndipo pamene Saulo atakhazikitsa ufumu wa pa Israele, iye anaponyana ndi adani ake onse pozungulira ponse, ndi Mowabu, ndi ana a Amoni, ndi Edomu ndi mafumu a Zoba, ndi Afilisti; ndipo paliponse anapotolokerapo, anawalanga.


Pamenepo Afilisti anasonkhanitsa makamu ao a nkhondo, naunjikana ku Soko wa ku Yuda, namanga zithando pakati pa Soko ndi Azeka ku Efesi-Damimu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa