1 Samueli 14:44 - Buku Lopatulika44 Pamenepo Saulo anati, Mulungu andilange, naonjezereko, pakuti udzafa ndithu, Yonatani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Pamenepo Saulo anati, Mulungu andilange, naonjezereko, pakuti udzafa ndithu, Yonatani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Apo Saulo adati, “Mulungu andilange ine, ngakhale kundipha kumene, ngati suufa iwe Yonatani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Sauli anati, “Mulungu andilange ngakhale kufa kumene, ngati sufa iwe Yonatani.” Onani mutuwo |