1 Samueli 14:40 - Buku Lopatulika40 Ndipo iye ananena ndi Aisraele onse, Inu mukhale mbali ina, ndipo ine ndi Yonatani mwana wanga tidzakhala mbali yinanso. Ndipo anthuwo ananena ndi Saulo, Chitani chimene chikukomerani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201440 Ndipo iye ananena ndi Aisraele onse, Inu mukhale mbali ina, ndipo ine ndi Yonatani mwana wanga tidzakhala mbali yinanso. Ndipo anthuwo ananena ndi Saulo, Chitani chimene chikukomerani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa40 Tsono adauza Aisraelewo kuti, “Inu mukhale mbali imodzi, ine ndi mwana wanga Yonatani tikhalanso mbali ina.” Anthuwo adauza Saulo kuti, “Muchite zimene zikukomereni.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero40 Tsono Sauli anawuza Aisraeli onse kuti, “Inu mukhale mbali imodzi. Ine ndi mwana wanga Yonatani tikhala mbali inayo.” “Chitani chilichonse chimene chikukomerani.” Onani mutuwo |