1 Samueli 14:29 - Buku Lopatulika29 Ndipo Yonatani anati, Atate wanga wavuta dziko; onani m'maso mwanga mwayera, chifukwa ndinalawako pang'ono uchiwu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201429 Ndipo Yonatani anati, Atate wanga wavuta dziko; onani m'maso mwanga mwayera, chifukwa ndinalawako pang'ono uchiwu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa29 Tsono Yonatani adati, “Bambo wanga wavutitsa anthu onse. Taonani ine m'maso mwanga mwayera, chifukwa ndalaŵako uchiwu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero29 Yonatani anati, “Abambo anga achita chinthu choyipira dziko. Taonani mʼmaso mwanga mwayera chifukwa ndalawa uchiwu pangʼono. Onani mutuwo |