1 Samueli 14:28 - Buku Lopatulika28 Ndipo wina wa anthuwo anayankha, nati, Atate wanu analangiza anthu kolimba ndi lumbiro, ndi kuti, Wotembereredwa iye wakudya lero chakudya. Ndipo anthuwo analema. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndipo wina wa anthuwo anayankha, nati, Atate wanu analangiza anthu kolimba ndi lumbiro, ndi kuti, Wotembereredwa iye wakudya lero chakudya. Ndipo anthuwo analema. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 Tsono mmodzi mwa anthuwo adati, “Bambo wanu waopseza anthu pakunena kuti, ‘Atembereredwe amene adye kanthu lero.’ Nchifukwa chake anthuŵa akuchita ngati akomoke ndi njala.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Kenaka mmodzi mwa Asilikali anamuwuza kuti, “Abambo ako alumbirira anthu nati, ‘Wotembereredwa munthu aliyense amene adye chakudya lero.’ Nʼchifukwa chake anthu alefuka.” Onani mutuwo |