1 Samueli 14:14 - Buku Lopatulika14 Kuwapha koyambako, Yonatani ndi wonyamula zida zake, anapha monga anthu makumi awiri, monga ndime ya munda yolima ng'ombe ziwiri tsiku limodzi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Kuwapha koyambako, Yonatani ndi wonyamula zida zake, anapha monga anthu makumi awiri, monga ndime ya munda yolima ng'ombe ziwiri tsiku limodzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Anthu amene Yonatani ndi mnyamata wake uja adapha nthaŵi yoyamba analipo ngati makumi aŵiri, ndipo adaŵaphera pa malo ochepa okwanira ngati theka la ekala. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Nthawi yoyambayo Yonatani ndi mnyamata wake uja anapha anthu makumi awiri ndipo anawaphera pa malo ochepa okwanira ngati theka la ekala. Onani mutuwo |