1 Samueli 13:9 - Buku Lopatulika9 Pamenepo Saulo anati, Andipatsire kuno nsembe yopsereza, ndi nsembe zoyamika. Ndipo iye anapereka nsembe yopserezayo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pamenepo Saulo anati, Andipatsire kuno nsembe yopsereza, ndi nsembe zoyamika. Ndipo iye anapereka nsembe yopserezayo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Choncho Saulo adati, “Bwera nayoni kuno nsembe yopserezayo pamodzi ndi nsembe zachiyanjano zija.” Ndipo Saulo adapereka nsembe yopsereza ija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Kotero iye anati, “Bwera nayoni nsembe yopsereza ndi nsembe ya chiyanjano.” Ndipo Sauli anapereka nsembe yopsereza. Onani mutuwo |