1 Samueli 13:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo kunali kuti pakutsiriza iye kupereka nsembe yopserezayo, pomwepo, onani, Samuele anafika. Ndipo Saulo anamchingamira kukamlonjera iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo kunali kuti pakutsiriza iye kupereka nsembe yopserezayo, pomwepo, onani, Samuele anafika. Ndipo Saulo anamchingamira kukamlonjera iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Atangomaliza kupereka nsembe yopserezayo, adangoona Samuele watulukira. Tsono Saulo adapita kukakumana naye ndi kumulonjera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Atangomaliza kupereka nsembe, anangoona Samueli watulukira ndipo Sauli anapita kukamulonjera. Onani mutuwo |