1 Samueli 13:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo iye anatsotsa masiku asanu ndi awiri, monga nthawi anampanga Samuele; koma Samuele sanafike ku Giligala, ndipo anthu anabalalika namsiya Saulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo iye anatsotsa masiku asanu ndi awiri, monga nthawi anampanga Samuele; koma Samuele sanafike ku Giligala, ndipo anthu anabalalika namsiya Saulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Sauloyo adadikira masiku asanu ndi aŵiri, monga momwe adaanenera Samuele. Koma Samueleyo sadafike ku Giligala, ndipo anthu adayamba kumthaŵira Saulo uja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Saulo anadikirira masiku asanu ndi awiri, monga mwa nthawi imene ananena Samueli. Koma Samueli sanabwere ku Giligala, ndipo anthu anayamba kumuthawa Sauli uja. Onani mutuwo |