1 Samueli 13:22 - Buku Lopatulika22 Chomwecho kunali kuti tsiku lankhondolo sunapezeke mkondo kapena lupanga m'manja a anthu onse anali ndi Saulo ndi Yonatani; koma Saulo yekha ndi Yonatani mwana wake anali nazo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Chomwecho kunali kuti tsiku lankhondolo sunapezeka mkondo kapena lupanga m'manja a anthu onse anali ndi Saulo ndi Yonatani; koma Saulo yekha ndi Yonatani mwana wake anali nazo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Motero tsiku lankhondolo panalibe lupanga kapena mkondo m'manja mwa Mwisraele aliyense amene ankatsata Saulo ndi Yonatani. Koma Saulo ndi mwana wake Yonatani, iwo okha ndiwo anali nazo zida. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Motero tsiku la nkhondolo panalibe lupanga kapena mkondo mʼdzanja la aliyense amene anatsatira Saulo ndi Yonatani. Koma Saulo ndi Yonatani, iwo okha ndiwo anali ndi zida. Onani mutuwo |