1 Samueli 13:21 - Buku Lopatulika21 ndipo mtengo wakukonza makasu, ndi zikhasu ndi makasu a mano unali masekeli awiri mwa atatu ndi mtengo wa nkhwangwazo; ndi kusongola zotwikira unali sekeli imodzi mwa atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 ndipo mtengo wakukonza makasu, ndi zikhasu ndi makasu a mano unali masekeli awiri mwa atatu ndi mtengo wa nkhwangwazo; ndi kusongola zotwikira unali sekeli imodzi mwa atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Mtengo wonoletsera nkhwangwa unali ndalama imodzi, ndipo mtengo wosanjitsira makasu ndi wosongoletsera zisonga unali ndalama ziŵiri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Mtengo wonolera mapulawo ndi makasu unali zigawo ziwiri za sekeli, mtengo wonolera zisonga ndi nkhwangwa unali gawo limodzi la Sekeli. Onani mutuwo |