1 Samueli 13:20 - Buku Lopatulika20 koma Aisraele onse ankatsikira kwa Afilisti, kuti awasanjire munthu yense chikhasu chake, cholimira chake, nkhwangwa yake, ndi chisenga chake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 koma Aisraele onse ankatsikira kwa Afilisti, kuti awasanjire munthu yense chikhasu chake, cholimira chake, nkhwangwa yake, ndi chisenga chake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Motero Mwisraele aliyense ankapita kwa Afilisti kukasanjitsa pulao kapena khasu lake, ndi kukanoletsa nkhwangwa yake kapena chikwakwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Kotero Aisraeli onse amapita kwa Afilisti kukanoletsa mapulawo, makasu, nkhwangwa ndi zikwakwa zawo. Onani mutuwo |