Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




1 Samueli 13:17 - Buku Lopatulika

17 Ndipo owawanya anatuluka ku zithando za Afilisti magulu atatu; gulu limodzi linalowa njira yonka ku Ofura, ku dera la Suwala;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndipo owawanya anatuluka ku zithando za Afilisti magulu atatu; gulu limodzi linalowa njira yonka ku Ofura, ku dera la Suwala;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Ankhondo a Filisti adatuluka kuchoka ku zithando zao m'magulu atatu. Gulu limodzi lidalunjika ku Ofura ku dziko la Suwala.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Ankhondo a Afilisti anatuluka mʼmisasa yawo mʼmagulu atatu. Gulu lina linapita ku Ofiri ku dziko la Suwala.

Onani mutuwo Koperani




1 Samueli 13:17
4 Mawu Ofanana  

ndi Avimu ndi Para, ndi Ofura;


ndi Hazara-Suwala, ndi Bala, ndi Ezemu;


Ndipo m'mawa mwake Saulo anagawa anthu magulu atatu; ndipo iwowa anafika pakati pa zithandozo mu ulonda wa mamawa, nakantha Aamoni kufikira kutentha kwa dzuwa. Ndipo otsalawo anabalalika, osatsala pamodzi ngakhale awiri.


Ndipo kunali kunthunthumira kuzithando, kuthengoko, ndi pakati pa anthu onse; a ku kaboma ndi owawanya omwe ananthunthumira; ndi dziko linagwedezeka; chomwecho kunali kunthunthumira kwakukulu koposa.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa